-
Salimo 69:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Anthu onse amene akuyembekezera inu asachite manyazi chifukwa cha ine,
Inu Ambuye Wamkulu Koposa, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
Anthu amene akufunafuna inu, asachite manyazi chifukwa cha ine,
Inu Mulungu wa Isiraeli.
-