Salimo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi pamene ndikukuitanani.+ Anthu oipa achite manyazi.+Apite ku Manda* ndipo akhale chete.+
17 Inu Yehova, musalole kuti ndichite manyazi pamene ndikukuitanani.+ Anthu oipa achite manyazi.+Apite ku Manda* ndipo akhale chete.+