Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 89:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mukamalamulira, nthawi zonse mumachita zinthu mwachilungamo komanso molungama.+

      Nthawi zonse mumasonyeza kukhulupirika komanso chikondi chokhulupirika.+

  • Miyambo 6:16-19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.

      Zilipo zinthu 7 zimene amanyansidwa nazo:

      17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja amene amakhetsa magazi a anthu osalakwa,+

      18 Mtima umene umakonza ziwembu,+ mapazi othamangira kukachita zoipa,

      19 Mboni yachinyengo imene nthawi zonse imanena mabodza,+

      Komanso aliyense amene amayambitsa mikangano pakati pa abale.+

  • Habakuku 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Maso anu ndi oyera kwambiri moti simungaonerere zinthu zoipa,

      Ndipo simungalekerere khalidwe loipa.+

      Ndiye nʼchifukwa chiyani mukulekerera anthu achinyengo,+

      Komanso mukukhala chete pamene munthu woipa akumeza munthu wolungama kuposa iyeyo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena