Salimo 103:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza chikondi chake chokhulupirika mpaka kalekaleKwa anthu amene amamuopa,+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+ Salimo 136:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 136 Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.+
17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza chikondi chake chokhulupirika mpaka kalekaleKwa anthu amene amamuopa,+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+ Salimo 136:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 136 Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.+
136 Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.+