Ekisodo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse, ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kumukomera mtima ndidzamukomera mtima, ndipo amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo.”+ Salimo 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi ndikanakhala ndili kuti ndikanapanda kukhala ndi chikhulupiriroChoti ndidzaona ubwino wa Yehova mʼdziko la anthu amoyo?*+
19 Koma Mulungu anati: “Ineyo ndidzakuonetsa ubwino wanga wonse, ndipo ndidzalengeza dzina langa lakuti Yehova kwa iwe.+ Amene ndikufuna kumukomera mtima ndidzamukomera mtima, ndipo amene ndikufuna kumusonyeza chifundo, ndidzamusonyeza chifundo.”+
13 Kodi ndikanakhala ndili kuti ndikanapanda kukhala ndi chikhulupiriroChoti ndidzaona ubwino wa Yehova mʼdziko la anthu amoyo?*+