Deuteronomo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Awa ndi mawu a pangano limene Yehova analamula Mose kuti achite ndi Aisiraeli mʼdziko la Mowabu, kuwonjezera pa pangano limene anachita nawo ku Horebe.+
29 Awa ndi mawu a pangano limene Yehova analamula Mose kuti achite ndi Aisiraeli mʼdziko la Mowabu, kuwonjezera pa pangano limene anachita nawo ku Horebe.+