Salimo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah) Salimo 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikhululukireni* machimo anga,+Ndipo fufutani* zolakwa zanga zonse.+
5 Pamapeto pake ndinaulula tchimo langa kwa inu,Sindinabise cholakwa changa.+ Ndinati: “Ndidzaulula machimo anga kwa Yehova.”+ Ndipo inu munandikhululukira zolakwa zanga ndi machimo anga.+ (Selah)