Salimo 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yembekezera Yehova ndi kutsatira njira zake,Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi. Oipa akamadzaphedwa,+ iwe udzaona.+
34 Yembekezera Yehova ndi kutsatira njira zake,Ndipo adzakukweza kuti ulandire dziko lapansi. Oipa akamadzaphedwa,+ iwe udzaona.+