Yeremiya 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Sindikhala pansi ndi gulu la anthu okonda zosangalatsa nʼkumasangalala nawo.+ Ndimakhala ndekha chifukwa dzanja lanu lili pa ine,Popeza mwandidzaza ndi mkwiyo.*+
17 Sindikhala pansi ndi gulu la anthu okonda zosangalatsa nʼkumasangalala nawo.+ Ndimakhala ndekha chifukwa dzanja lanu lili pa ine,Popeza mwandidzaza ndi mkwiyo.*+