1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+ Miyambo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzakhala wotetezeka,+Koma munthu wochita zinthu mwachinyengo adzadziwika.+
9 Amateteza mapazi a okhulupirika ake,+Koma anthu oipa adzawakhalitsa chete mumdima,+Popeza munthu sapambana chifukwa cha mphamvu zake.+
9 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzakhala wotetezeka,+Koma munthu wochita zinthu mwachinyengo adzadziwika.+