1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+ 2 Samueli 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa. Salimo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+ Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,Pomupulumutsa modabwitsa ndi dzanja lake lamanja.+
13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+
3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa.
6 Tsopano ndadziwa kuti Yehova amapulumutsa wodzozedwa wake.+ Amamuyankha kuchokera kumwamba kwake koyera,Pomupulumutsa modabwitsa ndi dzanja lake lamanja.+