Yesaya 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndidzachititsa kuti kumwamba kunjenjemere,Ndipo dziko lapansi lidzagwedezeka nʼkuchoka mʼmalo mwake+Chifukwa cha ukali wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake. Aheberi 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa nthawiyo, mawu ake anagwedeza dziko lapansi,+ koma tsopano walonjeza kuti: “Ndidzagwedezanso kumwamba, osati dziko lapansi lokha.”+
13 Choncho ndidzachititsa kuti kumwamba kunjenjemere,Ndipo dziko lapansi lidzagwedezeka nʼkuchoka mʼmalo mwake+Chifukwa cha ukali wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, pa tsiku limene mkwiyo wake udzayake.
26 Pa nthawiyo, mawu ake anagwedeza dziko lapansi,+ koma tsopano walonjeza kuti: “Ndidzagwedezanso kumwamba, osati dziko lapansi lokha.”+