Numeri 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo.
26 Iwo anabwerera kwa Mose ndi Aroni ndiponso gulu lonse la Aisiraeli mʼchipululu cha Parana, ku Kadesi.+ Anafotokozera gulu lonselo za ulendo wawo nʼkuwaonetsa zipatso za kudzikolo.