Salimo 22:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makolo athu ankadalira inu.+Iwo ankakudalirani ndipo inu munkawapulumutsa.+ 5 Iwo ankafuulira inu ndipo munkawapulumutsa.Ankakudalirani ndipo simunawakhumudwitse.*+ Aroma 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Paja lemba lina limati: “Palibe wokhulupirira iye amene adzakhumudwe.”+
4 Makolo athu ankadalira inu.+Iwo ankakudalirani ndipo inu munkawapulumutsa.+ 5 Iwo ankafuulira inu ndipo munkawapulumutsa.Ankakudalirani ndipo simunawakhumudwitse.*+