2 Samueli 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo+ ndiponso Wondipulumutsa.+