Salimo 71:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musanditaye pa nthawi imene ndakalamba.+Musandisiye pa nthawi imene mphamvu zanga zatha.+