Salimo 57:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndazunguliridwa ndi mikango.+Ndikuyenera kugona pakati pa anthu amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+
4 Ndazunguliridwa ndi mikango.+Ndikuyenera kugona pakati pa anthu amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+