Salimo 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinati: “Inu Yehova, ndikomereni mtima.+ Ndichiritseni,+ chifukwa ndakuchimwirani.”+ Salimo 103:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Moyo wanga utamande Yehova,Ndisaiwale zinthu zonse zimene wachita.+ 3 Iye amakukhululukira zolakwa zako zonse+Ndipo amachiritsa matenda ako onse.+
2 Moyo wanga utamande Yehova,Ndisaiwale zinthu zonse zimene wachita.+ 3 Iye amakukhululukira zolakwa zako zonse+Ndipo amachiritsa matenda ako onse.+