Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mumapulumutsa anthu odzichepetsa,+

      Koma mumanyansidwa ndi anthu odzikweza ndipo mumawatsitsa.+

  • Yesaya 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Maso odzikuza a munthu adzatsitsidwa,

      Ndipo anthu odzikweza adzachititsidwa manyazi.

      Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe tsiku limenelo.

  • Yakobo 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komabe, kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu amapereka kumaposa khalidwe limeneli. Nʼchifukwa chake lemba limati: “Mulungu amatsutsa odzikuza,+ koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena