Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyera.+Ali ngati siliva woyengedwa mungʼanjo yadothi nthawi zokwanira 7.