Malaki 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sakumutumikira.” Mateyu 13:49, 50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndi mmenenso zidzakhalire pamapeto a nthawi* ino. Angelo adzapita nʼkukachotsa oipa pakati pa olungama 50 ndipo adzawaponya mungʼanjo yamoto. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.
18 Ndipo mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sakumutumikira.”
49 Ndi mmenenso zidzakhalire pamapeto a nthawi* ino. Angelo adzapita nʼkukachotsa oipa pakati pa olungama 50 ndipo adzawaponya mungʼanjo yamoto. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.