Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Konzani pulani, koma idzalephereka.

      Nenani zimene mukufuna, koma sizidzachitika,

      Chifukwa Mulungu ali nafe.*+

  • Yesaya 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Anthu a mu Iguputo adzadabwa kwambiri

      Ndipo ine ndidzasokoneza mapulani awo.+

      Iwo adzafunsira kwa milungu yopanda pake,

      Kwa anthu amatsenga, kwa olankhula ndi mizimu ndiponso kwa olosera zamʼtsogolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena