Salimo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ali mʼkachisi wake wopatulika.+ Mpando wachifumu wa Yehova uli kumwamba.+ Maso ake amaona, inde maso ake* amayangʼanitsitsa ana a anthu.+ Salimo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova amayangʼana ana a anthu,Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, ngati pali aliyense amene akufunafuna Yehova.+ Miyambo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maso a Yehova ali paliponse,Amaona anthu oipa ndi abwino omwe.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+
4 Yehova ali mʼkachisi wake wopatulika.+ Mpando wachifumu wa Yehova uli kumwamba.+ Maso ake amaona, inde maso ake* amayangʼanitsitsa ana a anthu.+
2 Koma kuchokera kumwamba, Yehova amayangʼana ana a anthu,Kuti aone ngati pali aliyense wozindikira, ngati pali aliyense amene akufunafuna Yehova.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+