Mateyu 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Osangalala ndi anthu amene amabweretsa mtendere+ chifukwa adzatchedwa ana a Mulungu. Aheberi 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.
14 Muziyesetsa kukhala mwamtendere ndi anthu onse,+ komanso kukhala oyera+ chifukwa ngati munthu si woyera, sadzaona Ambuye.