Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma ngati wina wamva mawu a lumbiro ili nʼkulankhula modzitama mumtima mwake kuti, ‘Ndikhala ndi mtendere ngakhale kuti ndikuyendabe motsatira zofuna za mtima wanga,’ zimene zidzachititse kuti aliyense woyandikana naye* awonongedwe, 20 Yehova sadzafuna kukhululukira munthu woteroyo.+ Mʼmalomwake, mkwiyo waukulu wa Yehova udzamuyakira, ndipo matemberero onse amene alembedwa mʼbuku ili adzamugwera,+ ndipo Yehova adzachotseratu dzina la munthuyo pansi pa thambo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena