Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mʼdziko lanu mudzapitirizabe kupezeka anthu osauka.+ Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti, ‘Muzikhala owolowa manja kwa mʼbale wanu wovutika komanso wosauka mʼdziko lanu.’+

  • Yobu 31:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ngati ndinakana kupatsa osauka zimene ankafuna,+

      Kapena kuchititsa kuti mkazi wamasiye amve chisoni,*+

  • Yobu 31:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mkono wanga ugwe* kuchoka mʼmalo mwake,

      Ndipo mkono wanga uthyoke pachigongono.*

  • Salimo 112:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Iye wagawira ena mowolowa manja, wapereka kwa anthu osauka.+

      צ [Tsade]

      Chilungamo chake chidzakhalapo mpaka kalekale.+

      ק [Qoph]

      Mphamvu zake zidzawonjezeka* chifukwa cha ulemerero.

  • Miyambo 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Amene amakomera mtima munthu wonyozeka akukongoza Yehova,+

      Ndipo adzamʼbwezera* zimene anachitazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena