Salimo 94:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova sadzataya anthu ake,+Kapena kusiya cholowa chake.+ Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho nthawi zonse muziika Ufumu ndi mfundo zolungama za Mulungu pamalo oyamba pa moyo wanu, ndipo iye adzakupatsani zinthu zina zonsezi.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+
33 Choncho nthawi zonse muziika Ufumu ndi mfundo zolungama za Mulungu pamalo oyamba pa moyo wanu, ndipo iye adzakupatsani zinthu zina zonsezi.+
5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+