Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 25:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Anthu amenewa adzachoka kupita kuchiwonongeko chosatha,*+ koma olungama kumoyo wosatha.”+

  • Chivumbulutso 21:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu akuti: “Taonani! Chihema cha Mulungu chili pakati pa anthu ndipo iye azidzakhala nawo. Iwo adzakhala anthu ake ndipo Mulunguyo adzakhala nawo.+ 4 Iye adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo+ ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira, kubuula kapena kupweteka.+ Zakalezo zapita.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena