Mateyu 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake.+ Aefeso 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mawu owola asamatuluke pakamwa panu,+ koma pazituluka mawu abwino okha kuti alimbikitse ena pakafunika kutero, kuti athandize anthu amene akumvetsera.+ Akolose 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthawi zonse mawu anu azisonyeza kuti ndinu okoma mtima ndipo azikhala okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire munthu aliyense.+
35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake.+
29 Mawu owola asamatuluke pakamwa panu,+ koma pazituluka mawu abwino okha kuti alimbikitse ena pakafunika kutero, kuti athandize anthu amene akumvetsera.+
6 Nthawi zonse mawu anu azisonyeza kuti ndinu okoma mtima ndipo azikhala okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire munthu aliyense.+