Salimo 139:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho kwa ine maganizo anu ndi ofunika kwambiri, inu Mulungu,+ Ndipo ndi ochuluka kwambiri.+ 18 Nditati ndiyese kuwawerenga, angakhale ochuluka kwambiri kuposa mchenga.+ Podzuka ndingakhale ndikuwawerengabe.*+
17 Choncho kwa ine maganizo anu ndi ofunika kwambiri, inu Mulungu,+ Ndipo ndi ochuluka kwambiri.+ 18 Nditati ndiyese kuwawerenga, angakhale ochuluka kwambiri kuposa mchenga.+ Podzuka ndingakhale ndikuwawerengabe.*+