Salimo 71:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngakhale kuti mwachititsa kuti ndikumane ndi mavuto komanso masoka ambiri,+Bwezeretsani mphamvu zanga.Nditulutseni mʼdzenje lakuya.*+
20 Ngakhale kuti mwachititsa kuti ndikumane ndi mavuto komanso masoka ambiri,+Bwezeretsani mphamvu zanga.Nditulutseni mʼdzenje lakuya.*+