Yona 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nditatsala pangʼono kufa, ndinakumbukira Yehova.+ Ndipo pemphero langa linafika kwa inu mʼkachisi wanu woyera.+
7 Nditatsala pangʼono kufa, ndinakumbukira Yehova.+ Ndipo pemphero langa linafika kwa inu mʼkachisi wanu woyera.+