Salimo 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, musasiye kundisonyeza chifundo. Chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu zizinditeteza nthawi zonse.+ Miyambo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa lamulolo ndi nyale,+Ndipo malangizo ndi kuwala,+Komanso kudzudzula kumene kumathandiza munthu kusintha ndi njira yakumoyo.+
11 Inu Yehova, musasiye kundisonyeza chifundo. Chikondi chanu chokhulupirika komanso choonadi chanu zizinditeteza nthawi zonse.+
23 Chifukwa lamulolo ndi nyale,+Ndipo malangizo ndi kuwala,+Komanso kudzudzula kumene kumathandiza munthu kusintha ndi njira yakumoyo.+