-
Oweruza 6:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma Gidiyoni anayankha kuti: “Pepani mbuyanga, ngati Yehova ali nafe, nʼchifukwa chiyani tikukumana ndi mavuto onsewa?+ Nanga ntchito zake zodabwitsa zimene makolo athu anatiuza zija zili kuti?+ Iwo anatiuza kuti, ‘Yehova ndi amene anatitulutsa ku Iguputo.’+ Koma tsopano Yehova watisiya,+ ndipo watipereka kwa Amidiyani.”
-