Deuteronomo 28:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anthu adzachita mantha akadzaona zimene zakuchitikirani ndipo mudzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu kumene Yehova akukuthamangitsirani.+ 2 Mbiri 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ineyo ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga. Ndidzachititsa anthu kuinyoza ndiponso kuinenera mawu achipongwe pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
37 Anthu adzachita mantha akadzaona zimene zakuchitikirani ndipo mudzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu kumene Yehova akukuthamangitsirani.+
20 ineyo ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga. Ndidzachititsa anthu kuinyoza ndiponso kuinenera mawu achipongwe pakati pa mitundu yonse ya anthu.+