Aroma 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Malemba amati: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+