Yesaya 54:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mapiri akhoza kuchotsedwa,Ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,Koma chikondi changa chokhulupirika sichidzachotsedwa pa iwe,+Ndipo pangano langa lamtendere silidzagwedezeka,”+ akutero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+
10 Mapiri akhoza kuchotsedwa,Ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,Koma chikondi changa chokhulupirika sichidzachotsedwa pa iwe,+Ndipo pangano langa lamtendere silidzagwedezeka,”+ akutero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+