Yoswa 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndakulamula kale kuti ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa, chifukwa Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene ungapite.”+ Yeremiya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo adzamenyana nawe ndithu,Koma sadzakugonjetsa,Chifukwa Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikupulumutse.’” Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pamenepa? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
9 Ndakulamula kale kuti ukhale wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usachite mantha kapena kuopa, chifukwa Yehova Mulungu wako ali nawe kulikonse kumene ungapite.”+
19 Iwo adzamenyana nawe ndithu,Koma sadzakugonjetsa,Chifukwa Yehova wanena kuti, ‘Ine ndili ndi iwe+ kuti ndikupulumutse.’”