Mika 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mapiri akuluakulu, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake.Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+Chifukwa Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake.Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+
2 Inu mapiri akuluakulu, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake.Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+Chifukwa Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake.Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+