Deuteronomo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu, ngakhale kumwamba kwa kumwambako* komanso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zonsezo ndi zake.+ Yobu 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi ndani anandipatsapo chinthu chilichonse kuti ndimubwezere?+ Chilichonse chimene chili pansi pa thambo ndi changa.+ 1 Akorinto 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chifukwa “dziko lapansi ndi zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova.”*+
14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu, ngakhale kumwamba kwa kumwambako* komanso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zonsezo ndi zake.+
11 Ndi ndani anandipatsapo chinthu chilichonse kuti ndimubwezere?+ Chilichonse chimene chili pansi pa thambo ndi changa.+