1 Atesalonika 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzithokoza pa chilichonse.+ Mulungu akufuna kuti muzichita zimenezi chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu. Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+
18 Muzithokoza pa chilichonse.+ Mulungu akufuna kuti muzichita zimenezi chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu.
15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+