Genesis 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼnyumba muno mulibe woyangʼanira woposa ine, ndipo mbuye wanga anaika chilichonse mʼmanja mwanga kupatulapo inuyo, chifukwa ndinu mkazi wake. Ndiye ndingachitirenji choipa chachikulu chonchi nʼkuchimwira Mulungu?”+ 2 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero, Davide anauza Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+
9 Mʼnyumba muno mulibe woyangʼanira woposa ine, ndipo mbuye wanga anaika chilichonse mʼmanja mwanga kupatulapo inuyo, chifukwa ndinu mkazi wake. Ndiye ndingachitirenji choipa chachikulu chonchi nʼkuchimwira Mulungu?”+
13 Zitatero, Davide anauza Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+