Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Yehova anauza Samueli kuti: “Usaganizire mmene akuonekera komanso kutalika kwake+ chifukwa ine ndamukana ameneyu. Chifukwatu mmene munthu amaonera si mmene Mulungu amaonera. Munthu amaona zooneka ndi maso, koma Yehova amaona mumtima.”+

  • 2 Mafumu 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Yehova, chonde ndikukupemphani kuti mukumbukire kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse komanso ndachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.

  • 1 Mbiri 29:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Inu Mulungu wanga, ine ndikudziwa bwino kuti mumafufuza mitima+ ndiponso kuti mumakonda anthu okhulupirika.+ Ineyo ndapereka zinthu zonsezi mwakufuna kwanga komanso ndi mtima wopanda chinyengo. Ndasangalala kwambiri kuona anthu anu ali apawa, akupereka zopereka zawo mwakufuna kwawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena