-
Esitere 6:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho Hamani anatenga chovala ndi hatchi, ndipo anaveka Moredikayi+ chovalacho. Kenako anamʼkweza pahatchiyo nʼkumuyendetsa mʼbwalo la mzinda, akufuula patsogolo pake kuti: “Izi ndi zimene timachitira munthu amene mfumu yafuna kumʼpatsa ulemu!” 12 Kenako, Moredikayi anabwerera kugeti la mfumu. Koma Hamani anapita kunyumba kwake mofulumira, akulira ndiponso ataphimba kumutu.
-