Miyambo 3:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga, zimenezi* zisachoke pamaso pako. Uteteze nzeru zopindulitsa ndiponso kuganiza bwino.22 Zidzakupatsa moyoKomanso zidzakhala zokongoletsera mʼkhosi mwako.
21 Mwana wanga, zimenezi* zisachoke pamaso pako. Uteteze nzeru zopindulitsa ndiponso kuganiza bwino.22 Zidzakupatsa moyoKomanso zidzakhala zokongoletsera mʼkhosi mwako.