Miyambo 1:20, 21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nzeru yeniyeni+ ikufuula mumsewu.+ Ikufuula mokweza mawu mʼmabwalo a mzinda.+ 21 Ikufuula pamphambano ya* misewu yodutsa anthu ambiri. Pamageti olowera mumzinda, ikunena kuti:+
20 Nzeru yeniyeni+ ikufuula mumsewu.+ Ikufuula mokweza mawu mʼmabwalo a mzinda.+ 21 Ikufuula pamphambano ya* misewu yodutsa anthu ambiri. Pamageti olowera mumzinda, ikunena kuti:+