Miyambo 2:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukapitiriza kuzifunafuna ngati siliva,+Ndi kuzifufuza ngati chuma chobisika,+ 5 Udzamvetsa tanthauzo la kuopa Yehova+Ndipo udzamudziwadi Mulungu.+
4 Ukapitiriza kuzifunafuna ngati siliva,+Ndi kuzifufuza ngati chuma chobisika,+ 5 Udzamvetsa tanthauzo la kuopa Yehova+Ndipo udzamudziwadi Mulungu.+