Genesis 1:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Mulungu ananena kuti: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi kuti madziwo+ alekane.” 7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi. Yobu 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anaika malire pakati pa thambo ndi nyanja,+Anaika malire pakati pa kuwala ndi mdima.
6 Kenako Mulungu ananena kuti: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi kuti madziwo+ alekane.” 7 Choncho Mulungu anapanga mlengalenga nʼkulekanitsa madzi kuti ena akhale pansi pa mlengalenga ndipo ena akhale pamwamba pa mlengalenga.+ Ndipo zinaterodi.