-
1 Mafumu 8:31, 32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Munthu akachimwira mnzake, wochimwiridwayo nʼkulumbiritsa* wochimwayo pofuna kutsimikiza kuti sanachimwedi, ndiyeno wochimwayo akabwera patsogolo pa guwa lansembe mʼnyumba muno,+ 32 inu mumve muli kumwamba ndipo muchitepo kanthu posonyeza amene ali wolakwa nʼkumubwezera mogwirizana ndi zochita zake komanso musonyeze amene ali wosalakwa nʼkumupatsa mphoto mogwirizana ndi chilungamo chake.+
-