Miyambo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu amene wapeza mkazi wabwino wapeza chinthu chabwino,+Ndipo Yehova amamukomera mtima.*+ Miyambo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nyumba komanso chuma ndi cholowa chochokera kwa makolo,Koma mkazi wanzeru amachokera kwa Yehova.+